Deuteronomo 5:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ndipo anthu inu muonetsetse kuti mukuchita monga mmene Yehova Mulungu wanu wakulamulirani.+ Musatembenukire kudzanja lamanja kapena lamanzere.+ Yohane 13:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ngati zimenezi mukuzidziwa, ndinu odala mukamazichita.+ Yakobo 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Komabe muzichita zimene mawu amanena,+ osati kungomva chabe, n’kumadzinyenga ndi maganizo onama.+
32 Ndipo anthu inu muonetsetse kuti mukuchita monga mmene Yehova Mulungu wanu wakulamulirani.+ Musatembenukire kudzanja lamanja kapena lamanzere.+