23 Atafika kuchigwa* cha Esikolo,+ anadula nthambi yokhala ndi tsango limodzi la mphesa,+ ndipo anthu awiri analinyamula paphewa ndi mitengo yonyamulira. Anatengakonso makangaza*+ ndi nkhuyu.
26 Iwo anabwera kwa Mose ndi Aroni, ndiponso kwa khamu lonse la ana a Isiraeli m’chipululu cha Parana, ku Kadesi.+ Anafotokozera onsewo za ulendo wawo n’kuwaonetsa zipatso za kudzikolo.