Deuteronomo 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 samala kuti usaiwale+ Yehova amene anakutulutsa m’dziko la Iguputo, m’nyumba yaukapolo.