Machitidwe 7:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Anauza Aroni kuti, ‘Tipangire milungu ititsogolere. Chifukwa sitikudziwa zimene zachitikira Mose, amene anatitsogolera potuluka m’dziko la Iguputo.’+
40 Anauza Aroni kuti, ‘Tipangire milungu ititsogolere. Chifukwa sitikudziwa zimene zachitikira Mose, amene anatitsogolera potuluka m’dziko la Iguputo.’+