Numeri 16:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Nthakayo inatsegula pakamwa pake n’kuwameza iwowo ndi mabanja awo, limodzi ndi anthu ena onse amene anali kumbali ya Kora, komanso katundu wawo yense.+
32 Nthakayo inatsegula pakamwa pake n’kuwameza iwowo ndi mabanja awo, limodzi ndi anthu ena onse amene anali kumbali ya Kora, komanso katundu wawo yense.+