Deuteronomo 28:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 “Ukamveradi mawu a Yehova Mulungu wako mwa kuonetsetsa kuti ukutsatira malamulo ake onse amene ndikukupatsa lero,+ Yehova Mulungu wako adzakukweza ndithu pamwamba pa mitundu yonse ya padziko lapansi.+ Salimo 19:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiponso mtumiki wanu amachenjezedwa nazo.+Munthu wosunga zigamulozo amapeza mphoto yaikulu.+ Yesaya 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mukakhala ndi mtima wofuna kundimvera, mudzadya zabwino za m’dziko lanu.+
28 “Ukamveradi mawu a Yehova Mulungu wako mwa kuonetsetsa kuti ukutsatira malamulo ake onse amene ndikukupatsa lero,+ Yehova Mulungu wako adzakukweza ndithu pamwamba pa mitundu yonse ya padziko lapansi.+