Deuteronomo 28:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Madalitso onsewa adzakutsata ndi kukupeza+ chifukwa ukumvera mawu a Yehova Mulungu wako: Yoweli 2:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pamenepo mudzadya ndi kukhuta+ ndipo mudzatamanda dzina la Yehova Mulungu wanu+ amene wakuchitirani zodabwitsa.+ Anthu anga sadzachita manyazi mpaka kalekale.*+
26 Pamenepo mudzadya ndi kukhuta+ ndipo mudzatamanda dzina la Yehova Mulungu wanu+ amene wakuchitirani zodabwitsa.+ Anthu anga sadzachita manyazi mpaka kalekale.*+