Deuteronomo 27:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Amene adzaimirira kuti avomere pamene matemberero+ akutchulidwa paphiri la Ebala+ ndi awa: Rubeni, Gadi, Aseri, Zebuloni, Dani ndi Nafitali. Yoswa 8:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Pambuyo pake, Yoswa anawerenga mokweza mawu onse a chilamulo,+ madalitso+ ndi matemberero,+ malinga ndi zonse zolembedwa m’buku la chilamulo.
13 Amene adzaimirira kuti avomere pamene matemberero+ akutchulidwa paphiri la Ebala+ ndi awa: Rubeni, Gadi, Aseri, Zebuloni, Dani ndi Nafitali.
34 Pambuyo pake, Yoswa anawerenga mokweza mawu onse a chilamulo,+ madalitso+ ndi matemberero,+ malinga ndi zonse zolembedwa m’buku la chilamulo.