Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 14:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Uwauze kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Pali ine Mulungu wamoyo, mudzandifunse ngati sindidzachita kwa inu monga mwa zimene mwakhala mukulankhula, zimene ndadzimvera ndekha m’makutu mwangamu.+

  • Numeri 14:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 “‘“Ine Yehova ndalankhula, mudzandifunse ngati sindidzawafafaniza m’chipululu mommuno anthu oipa onsewa,+ amene agwirizana kuti atsutsane ndi ine. Onse adzathera m’chipululu mommuno.+

  • Numeri 32:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pa tsiku limenelo Yehova anakwiya koopsa, ndipo analumbira+ kuti,

  • Deuteronomo 2:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ndipo masiku amene tinayenda kuchokera ku Kadesi-barinea mpaka kuwoloka chigwa cha Zeredi anali zaka 38, kufikira m’badwo wa amuna otha kupita kunkhondo utatha pakati panu, monga mmene Yehova analumbirira kwa iwo.+

  • Salimo 95:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Kunena za anthu amenewa ndinalumbira mu mkwiyo wanga kuti:+

      “Sadzalowa mu mpumulo wanga.”+

  • Aheberi 3:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Choncho ndinalumbira mu mkwiyo wanga kuti, ‘Sadzalowa+ mu mpumulo wanga.’”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena