Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 14:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Ana anu adzakhala abusa m’chipululu+ kwa zaka 40, ndipo adzavutika chifukwa cha kusakhulupirika*+ kwanu, mpaka womalizira kufa wa inu atagona m’manda m’chipululu.+

  • Numeri 32:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 ‘Amuna amene anatuluka mu Iguputo kuyambira azaka 20 kupita m’tsogolo,+ sadzaiona nthaka imene ndinalumbirira Abulahamu, Isaki ndi Yakobo,+ chifukwa sanandimvere ndi mtima wonse.

  • Deuteronomo 1:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 ‘Palibe munthu ndi mmodzi yemwe mwa anthu a m’badwo woipa uwu amene adzaona dziko labwino limene ndinalumbira kuti ndidzalipereka kwa makolo anu,+

  • Salimo 95:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Kunena za anthu amenewa ndinalumbira mu mkwiyo wanga kuti:+

      “Sadzalowa mu mpumulo wanga.”+

  • Salimo 106:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Choncho Mulungu anawalumbirira atakweza dzanja lake,+

      Kuti adzawapha m’chipululu,+

  • Ezekieli 20:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ine ndinakweza dzanja langa powalumbirira m’chipululu+ kuti sindidzawalowetsa m’dziko limene ndinawapatsa, dziko loyenda mkaka ndi uchi,+ (dziko lokongola kwambiri kuposa mayiko onse)+

  • Aheberi 3:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Nanga kodi analumbirira+ ndani kuti sadzalowa mu mpumulo wake? Kodi si omwe aja amene anachita zosamvera?+

  • Yuda 5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ngakhale kuti mukudziwa kale zinthu zonse, ndikufuna kukukumbutsani kuti,+ ngakhale kuti Yehova anapulumutsa anthu ake powatulutsa m’dziko la Iguputo,+ pambuyo pake anawononga amene analibe chikhulupiriro.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena