Deuteronomo 14:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 mbawala yamphongo, insa, ngondo,+ mbuzi yakuthengo, mphalapala, nkhosa yakuthengo ndi chinkhoma. Deuteronomo 15:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Uzimudyera mumzinda wanu ngati mmene umadyera insa ndi mbawala yamphongo.+ Nayenso munthu wodetsedwa komanso munthu woyera azidya.+
22 Uzimudyera mumzinda wanu ngati mmene umadyera insa ndi mbawala yamphongo.+ Nayenso munthu wodetsedwa komanso munthu woyera azidya.+