Levitiko 11:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Musadyeko nyama iliyonse ya zimenezi, ndipo nyamazi zikafa musamazikhudze.+ Zikhale zodetsedwa kwa inu.+
8 Musadyeko nyama iliyonse ya zimenezi, ndipo nyamazi zikafa musamazikhudze.+ Zikhale zodetsedwa kwa inu.+