Ekisodo 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “‘Adzadye nyamayo usiku umenewu.+ Idzakhale yowotcha ndipo adzaidye pamodzi ndi mikate yopanda chofufumitsa+ ndi masamba owawa.+ 2 Mbiri 35:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kenako anaphika+ nsembe ya pasika+ pamoto malinga ndi mwambo wawo ndipo zinthu zopatulika anaziphika+ m’miphika, m’miphika ya pansi pozungulira ndi m’miphika yosalowa kwambiri. Atatero anapititsa nyamayo msangamsanga kwa ana onse a anthuwo.+
8 “‘Adzadye nyamayo usiku umenewu.+ Idzakhale yowotcha ndipo adzaidye pamodzi ndi mikate yopanda chofufumitsa+ ndi masamba owawa.+
13 Kenako anaphika+ nsembe ya pasika+ pamoto malinga ndi mwambo wawo ndipo zinthu zopatulika anaziphika+ m’miphika, m’miphika ya pansi pozungulira ndi m’miphika yosalowa kwambiri. Atatero anapititsa nyamayo msangamsanga kwa ana onse a anthuwo.+