2 Mbiri 35:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Zitatero anaphika* nsembe ya Pasika pamoto malinga ndi mwambo wawo.+ Nsembe zopatulika anaziphikira mʼmiphika ingʼonoingʼono, mʼmiphika ikuluikulu ndi mʼmapani. Atamaliza kuphika anapititsa nyamayo mofulumira kwa anthu ena onse.
13 Zitatero anaphika* nsembe ya Pasika pamoto malinga ndi mwambo wawo.+ Nsembe zopatulika anaziphikira mʼmiphika ingʼonoingʼono, mʼmiphika ikuluikulu ndi mʼmapani. Atamaliza kuphika anapititsa nyamayo mofulumira kwa anthu ena onse.