Deuteronomo 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 koma mudzafunefune malo amene Yehova Mulungu wanu adzasankhe pakati pa mafuko anu onse kuti aikepo dzina lake, kuti lizikhala pamenepo. Amenewo ndiwo malo amene muzidzapitako.+ Salimo 122:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mapazi athu anaima+Pazipata zako iwe Yerusalemu.+ Salimo 122:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kumeneko n’kumene kumakhala mipando yachiweruzo,+Mipando yachifumu ya nyumba ya Davide.+
5 koma mudzafunefune malo amene Yehova Mulungu wanu adzasankhe pakati pa mafuko anu onse kuti aikepo dzina lake, kuti lizikhala pamenepo. Amenewo ndiwo malo amene muzidzapitako.+