Numeri 18:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Chakhumi chimene ana a Isiraeli azipereka kwa Yehova monga chopereka, ndawapatsa Alevi monga cholowa chawo. N’chifukwa chake ndinawauza kuti, ‘Asalandire cholowa pakati pa ana a Isiraeli.’”+ Deuteronomo 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 N’chifukwa chake Levi alibe gawo ndiponso cholowa+ monga abale ake. Yehova ndiye cholowa chake, monga mmene Yehova Mulungu wanu anamuuzira.+ Yoswa 13:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Fuko la Alevi, Mose sanalipatse cholowa cha malo.+ Yehova Mulungu wa Isiraeli ndiye cholowa chawo, monga mmene anawalonjezera.+
24 Chakhumi chimene ana a Isiraeli azipereka kwa Yehova monga chopereka, ndawapatsa Alevi monga cholowa chawo. N’chifukwa chake ndinawauza kuti, ‘Asalandire cholowa pakati pa ana a Isiraeli.’”+
9 N’chifukwa chake Levi alibe gawo ndiponso cholowa+ monga abale ake. Yehova ndiye cholowa chake, monga mmene Yehova Mulungu wanu anamuuzira.+
33 Fuko la Alevi, Mose sanalipatse cholowa cha malo.+ Yehova Mulungu wa Isiraeli ndiye cholowa chawo, monga mmene anawalonjezera.+