Ezekieli 21:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mfumu ya Babulo yaima chilili pamene panakumana misewu iwiri kuti iwombeze maula.+ Mfumuyo yagwedeza mivi, yafunsira kwa aterafi*+ ndi kuyang’ana pachiwindi cha nyama.
21 Mfumu ya Babulo yaima chilili pamene panakumana misewu iwiri kuti iwombeze maula.+ Mfumuyo yagwedeza mivi, yafunsira kwa aterafi*+ ndi kuyang’ana pachiwindi cha nyama.