Yoswa 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Tenga amuna 12 pakati pa anthuwa, mwamuna mmodzi pafuko lililonse.+ Machitidwe 26:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndipo mafuko athu 12 akuyembekezera kuona kukwaniritsidwa kwa lonjezo limeneli, mwa kumuchitira utumiki wopatulika mosalekeza usana ndi usiku.+ Chotero Mfumu, Ayuda akundiimba mlandu chifukwa cha chiyembekezo chimenechi.+
7 Ndipo mafuko athu 12 akuyembekezera kuona kukwaniritsidwa kwa lonjezo limeneli, mwa kumuchitira utumiki wopatulika mosalekeza usana ndi usiku.+ Chotero Mfumu, Ayuda akundiimba mlandu chifukwa cha chiyembekezo chimenechi.+