Yoswa 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Gawo+ la fuko la ana a Yuda potsata mabanja awo linkafika kumalire a Edomu,+ ndi kuchipululu cha Zini,+ mpaka kothera kwa Negebu,+ kum’mwera. 1 Mbiri 6:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 anapatsidwa mzinda wa Heburoni+ m’dziko la Yuda, ndi malo ake odyetserako ziweto kuzungulira mzinda wonsewo.
15 Gawo+ la fuko la ana a Yuda potsata mabanja awo linkafika kumalire a Edomu,+ ndi kuchipululu cha Zini,+ mpaka kothera kwa Negebu,+ kum’mwera.
55 anapatsidwa mzinda wa Heburoni+ m’dziko la Yuda, ndi malo ake odyetserako ziweto kuzungulira mzinda wonsewo.