Ekisodo 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ana a Gerisoni anali Libini ndi Simeyi,+ malinga ndi mzere wobadwira wa makolo awo.+ Numeri 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Amene anawerengedwa anali amuna onse kuyambira amwezi umodzi kupita m’tsogolo.+ Onse owerengedwa anakwana 7,500.+ 1 Mbiri 6:62 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 62 Ana a Gerisomu+ potsata mabanja awo anapatsidwa mizinda kuchokera ku fuko la Isakara,+ fuko la Aseri,+ fuko la Nafitali,+ ndi fuko la Manase+ ku Basana. Anapatsidwa mizinda 13.
22 Amene anawerengedwa anali amuna onse kuyambira amwezi umodzi kupita m’tsogolo.+ Onse owerengedwa anakwana 7,500.+
62 Ana a Gerisomu+ potsata mabanja awo anapatsidwa mizinda kuchokera ku fuko la Isakara,+ fuko la Aseri,+ fuko la Nafitali,+ ndi fuko la Manase+ ku Basana. Anapatsidwa mizinda 13.