Yoswa 10:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Zitatero, Yoswa ndi Aisiraeli onse amene anali naye anachoka ku Makeda n’kupita ku Libina+ komwe anakachitako nkhondo. Yoswa 15:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Libina,+ Eteri,+ Asani, Yesaya 37:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Rabisake+ anali atamva kuti mfumu ya Asuri yachoka ku Lakisi,+ choncho anabwerera kwa mfumuyo n’kukaipeza ikumenyana ndi Libina.+
29 Zitatero, Yoswa ndi Aisiraeli onse amene anali naye anachoka ku Makeda n’kupita ku Libina+ komwe anakachitako nkhondo.
8 Rabisake+ anali atamva kuti mfumu ya Asuri yachoka ku Lakisi,+ choncho anabwerera kwa mfumuyo n’kukaipeza ikumenyana ndi Libina.+