1 Mbiri 6:71 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 71 Kuchokera ku banja la hafu ya fuko la Manase, anapatsa ana a Gerisomu+ mzinda wa Golani+ ku Basana ndi malo ake odyetserako ziweto, ndiponso mzinda wa Asitaroti+ ndi malo ake odyetserako ziweto.
71 Kuchokera ku banja la hafu ya fuko la Manase, anapatsa ana a Gerisomu+ mzinda wa Golani+ ku Basana ndi malo ake odyetserako ziweto, ndiponso mzinda wa Asitaroti+ ndi malo ake odyetserako ziweto.