Yoswa 21:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ana a Merari+ anapatsidwa mizinda 12 yochokera m’fuko la Rubeni,+ Gadi,+ ndi Zebuloni,+ potsata mabanja awo. 1 Mbiri 6:77 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 77 Kuchokera ku fuko la Zebuloni,+ anapatsa ana a Merari amene anatsala, mzinda wa Rimono+ ndi malo ake odyetserako ziweto, ndiponso mzinda wa Tabori ndi malo ake odyetserako ziweto.
7 Ana a Merari+ anapatsidwa mizinda 12 yochokera m’fuko la Rubeni,+ Gadi,+ ndi Zebuloni,+ potsata mabanja awo.
77 Kuchokera ku fuko la Zebuloni,+ anapatsa ana a Merari amene anatsala, mzinda wa Rimono+ ndi malo ake odyetserako ziweto, ndiponso mzinda wa Tabori ndi malo ake odyetserako ziweto.