Miyambo 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kuyankha modekha kumabweza mkwiyo,+ koma mawu opweteka amayambitsa mkwiyo.+ Miyambo 18:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Woyamba kufotokoza mbali yake pa mlandu amaoneka ngati wolondola,+ koma mnzake amabwera n’kumufufuzafufuza.+
17 Woyamba kufotokoza mbali yake pa mlandu amaoneka ngati wolondola,+ koma mnzake amabwera n’kumufufuzafufuza.+