Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 18:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Ndipo Mose anasankha amuna oyenerera mu Isiraeli yense ndi kuwapatsa udindo wokhala atsogoleri a anthu,+ kuti akhale atsogoleri a magulu a anthu 1,000, atsogoleri a magulu a anthu 100, atsogoleri a magulu a anthu 50 ndi atsogoleri a magulu a anthu 10.

  • Numeri 1:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Amenewa ndiwo osankhidwa a khamu la anthuwo, atsogoleri a mafuko+ a makolo awo. Aliyense wa iwo ndi mtsogoleri wa anthu masauzande mu Isiraeli.”+

  • Yoswa 23:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Pa nthawiyo, Yoswa anaitana Aisiraeli onse+ ndi akulu awo, omwe anali atsogoleri awo, oweruza awo, ndi akapitawo awo,+ n’kuwauza kuti: “Ine ndakalamba ndipo ndili ndi zaka zambiri.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena