Genesis 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano Yehova anauza Abulamu kuti: “Tuluka m’dziko lako, pakati pa abale ako, ndi kusiya nyumba ya bambo ako. Upite kudziko limene ndidzakusonyeza.+ Nehemiya 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Inu ndinu Yehova Mulungu woona, amene munasankha Abulamu+ ndi kum’tulutsa ku Uri wa Akasidi+ ndipo munamutcha dzina lakuti Abulahamu.+ Machitidwe 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Sitefano anati: “Amuna inu, abale anga ndi abambo anga, mvetserani! Mulungu waulemerero+ anaonekera kwa kholo lathu Abulahamu pamene anali ku Mesopotamiya, asanakakhale ku Harana.+
12 Tsopano Yehova anauza Abulamu kuti: “Tuluka m’dziko lako, pakati pa abale ako, ndi kusiya nyumba ya bambo ako. Upite kudziko limene ndidzakusonyeza.+
7 Inu ndinu Yehova Mulungu woona, amene munasankha Abulamu+ ndi kum’tulutsa ku Uri wa Akasidi+ ndipo munamutcha dzina lakuti Abulahamu.+
2 Sitefano anati: “Amuna inu, abale anga ndi abambo anga, mvetserani! Mulungu waulemerero+ anaonekera kwa kholo lathu Abulahamu pamene anali ku Mesopotamiya, asanakakhale ku Harana.+