Genesis 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Odalitsa iwe ndidzawadalitsa, ndipo otemberera iwe ndidzawatemberera.+ Mabanja onse a padziko lapansi adzapeza madalitso* chifukwa cha iwe.”+ Numeri 25:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Amuna inu, athireni nkhondo Amidiyani, ndipo muwakanthe,+ Numeri 31:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Amunawo anakathira nkhondo Amidiyani, monga mmene Yehova analamulira Mose, ndipo anapha mwamuna aliyense.+ Numeri 31:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Atafika kwa Mose anati: “Atumiki anufe tawerenga amuna onse ankhondo amene tikuwayang’anira, ndipo palibe ndi mmodzi yemwe amene akusowapo.+
3 Odalitsa iwe ndidzawadalitsa, ndipo otemberera iwe ndidzawatemberera.+ Mabanja onse a padziko lapansi adzapeza madalitso* chifukwa cha iwe.”+
7 Amunawo anakathira nkhondo Amidiyani, monga mmene Yehova analamulira Mose, ndipo anapha mwamuna aliyense.+
49 Atafika kwa Mose anati: “Atumiki anufe tawerenga amuna onse ankhondo amene tikuwayang’anira, ndipo palibe ndi mmodzi yemwe amene akusowapo.+