Ekisodo 15:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pamenepo mafumu a ku Edomu adzasokonezeka.Ndipo olamulira amphamvu a ku Mowabu adzanjenjemera ndi mantha.+Ndithu, anthu onse okhala mu Kanani adzataya mtima.+ Yoswa 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndipo iye anauza amunawo kuti: “Ndikudziwa kuti Yehova akupatsani ndithu dziko lino.+ Ife tagwidwa ndi mantha chifukwa cha inu,+ ndipo anthu a dziko lino ataya mtima chifukwa chokuopani.+ Yoswa 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Titangomva zimenezi, mitima yathu inayamba kusungunuka ndi mantha,+ ndipo mpaka pano palibe aliyense amene akulimba mtima, chifukwa choopa inu.+ Ndithu, Yehova Mulungu wanu ndiye Mulungu wa kumwamba ndi padziko lapansi.+
15 Pamenepo mafumu a ku Edomu adzasokonezeka.Ndipo olamulira amphamvu a ku Mowabu adzanjenjemera ndi mantha.+Ndithu, anthu onse okhala mu Kanani adzataya mtima.+
9 Ndipo iye anauza amunawo kuti: “Ndikudziwa kuti Yehova akupatsani ndithu dziko lino.+ Ife tagwidwa ndi mantha chifukwa cha inu,+ ndipo anthu a dziko lino ataya mtima chifukwa chokuopani.+
11 Titangomva zimenezi, mitima yathu inayamba kusungunuka ndi mantha,+ ndipo mpaka pano palibe aliyense amene akulimba mtima, chifukwa choopa inu.+ Ndithu, Yehova Mulungu wanu ndiye Mulungu wa kumwamba ndi padziko lapansi.+