Deuteronomo 26:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Inu lero mwachititsa Yehova kunena kuti adzakhala Mulungu wanu mukamayenda m’njira zake ndi kusunga malangizo,+ malamulo+ ndi zigamulo zake+ ndiponso kumvera mawu ake.+ Mlaliki 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ukalonjeza kwa Mulungu usamachedwe kukwaniritsa lonjezo lako,+ chifukwa palibe amene amasangalala ndi anthu opusa.+ Uzikwaniritsa zinthu zimene walonjeza.+
17 Inu lero mwachititsa Yehova kunena kuti adzakhala Mulungu wanu mukamayenda m’njira zake ndi kusunga malangizo,+ malamulo+ ndi zigamulo zake+ ndiponso kumvera mawu ake.+
4 Ukalonjeza kwa Mulungu usamachedwe kukwaniritsa lonjezo lako,+ chifukwa palibe amene amasangalala ndi anthu opusa.+ Uzikwaniritsa zinthu zimene walonjeza.+