Yoswa 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ansembewo akadzaliza malipenga a nyanga za nkhosa, ndipo inu mukadzamva kulira kwa malipengawo, nonse mudzafuule mfuu yankhondo mwamphamvu,+ ndipo mpanda wonse wa mzindawo udzagwa pansi.+ Pamenepo, nonsenu mudzathamangire kumeneko.” Yoswa 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Yoswa analamula asilikaliwo+ kuti: “Musafuule kapena kulankhula kanthu, ndipo pakamwa panu pasatuluke mawu alionse kufikira tsiku limene ndidzakuuzani kuti, ‘Fuulani!’ Pamenepo mudzafuule.”+ 2 Mbiri 13:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kenako amuna a Yuda anayamba kufuula mfuu ya nkhondo.+ Atafuula mfuu ya nkhondoyo, Mulungu woona anagonjetsa+ Yerobowamu ndi Aisiraeli onse pamaso pa Abiya+ ndi Ayuda.
5 Ansembewo akadzaliza malipenga a nyanga za nkhosa, ndipo inu mukadzamva kulira kwa malipengawo, nonse mudzafuule mfuu yankhondo mwamphamvu,+ ndipo mpanda wonse wa mzindawo udzagwa pansi.+ Pamenepo, nonsenu mudzathamangire kumeneko.”
10 Yoswa analamula asilikaliwo+ kuti: “Musafuule kapena kulankhula kanthu, ndipo pakamwa panu pasatuluke mawu alionse kufikira tsiku limene ndidzakuuzani kuti, ‘Fuulani!’ Pamenepo mudzafuule.”+
15 Kenako amuna a Yuda anayamba kufuula mfuu ya nkhondo.+ Atafuula mfuu ya nkhondoyo, Mulungu woona anagonjetsa+ Yerobowamu ndi Aisiraeli onse pamaso pa Abiya+ ndi Ayuda.