Oweruza 20:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Pamenepo Isiraeli anaika amuna kuti abisalire+ mzinda wonse wa Gibeya. 2 Mbiri 13:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamenepo Yerobowamu anatumiza asilikali kuti akawabisalire kumbuyo, choncho Yerobowamuyo ndi asilikali ake anakhala kutsogolo kwa Ayuda ndipo obisalawo anali kumbuyo kwa Ayudawo.+
13 Pamenepo Yerobowamu anatumiza asilikali kuti akawabisalire kumbuyo, choncho Yerobowamuyo ndi asilikali ake anakhala kutsogolo kwa Ayuda ndipo obisalawo anali kumbuyo kwa Ayudawo.+