Yoswa 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Iwo anauza Yoswa kuti: “Yehova wapereka dziko lonselo m’manja mwathu.+ Ndipo anthu onse a m’dzikomo akuchita mantha chifukwa cha ife.”+ Miyambo 21:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Hatchi* anaikonzera tsiku la nkhondo,+ koma Yehova ndiye amapulumutsa.+
24 Iwo anauza Yoswa kuti: “Yehova wapereka dziko lonselo m’manja mwathu.+ Ndipo anthu onse a m’dzikomo akuchita mantha chifukwa cha ife.”+