Yoswa 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndipo mukakangoti mwalanda mzindawo, mukauyatse moto.+ Mukachite zimenezo malinga ndi mawu a Yehova. Izi n’zimene ndakulamulani.”+ Yoswa 8:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Chotero Yoswa anatentha mzinda wa Ai+ n’kuusiya uli bwinja lokhalapo mpaka kalekale, ndipo lilipobe mpaka lero.
8 Ndipo mukakangoti mwalanda mzindawo, mukauyatse moto.+ Mukachite zimenezo malinga ndi mawu a Yehova. Izi n’zimene ndakulamulani.”+
28 Chotero Yoswa anatentha mzinda wa Ai+ n’kuusiya uli bwinja lokhalapo mpaka kalekale, ndipo lilipobe mpaka lero.