-
Numeri 31:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 “Iweyo ndi wansembe Eleazara ndi atsogoleri a khamulo, mutenge zofunkha zonse, zomwe zikuphatikizapo anthu ndi ziweto.
-
-
Mlaliki 2:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Munthu wabwino pamaso pa Mulungu,+ Mulunguyo amam’patsa nzeru, kudziwa zinthu, ndi kusangalala.+ Koma wochimwa amam’patsa ntchito yotuta ndi kusonkhanitsa zinthu kuti azipereke kwa munthu amene ali wabwino pamaso pa Mulungu woona.+ Zimenezinso n’zachabechabe ndipo kuli ngati kuthamangitsa mphepo.+
-