Levitiko 24:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “‘Chigamulo chilichonse chigwire ntchito mofanana pakati panu, kwa mlendo wokhala pakati panu ndi kwa nzika,+ chifukwa ine ndine Yehova Mulungu wanu.’”+ Numeri 15:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pakhale malamulo ndi zigamulo zofanana kwa inu ndi kwa alendo amene akukhala nanu.’”+
22 “‘Chigamulo chilichonse chigwire ntchito mofanana pakati panu, kwa mlendo wokhala pakati panu ndi kwa nzika,+ chifukwa ine ndine Yehova Mulungu wanu.’”+