Deuteronomo 27:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Amene adzaimirira ndi kudalitsa anthu paphiri la Gerizimu+ mukawoloka Yorodano ndi awa: Simiyoni, Levi, Yuda, Isakara, Yosefe ndi Benjamini.
12 “Amene adzaimirira ndi kudalitsa anthu paphiri la Gerizimu+ mukawoloka Yorodano ndi awa: Simiyoni, Levi, Yuda, Isakara, Yosefe ndi Benjamini.