Deuteronomo 27:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Amene adzaimirira kuti avomere pamene matemberero+ akutchulidwa paphiri la Ebala+ ndi awa: Rubeni, Gadi, Aseri, Zebuloni, Dani ndi Nafitali.
13 Amene adzaimirira kuti avomere pamene matemberero+ akutchulidwa paphiri la Ebala+ ndi awa: Rubeni, Gadi, Aseri, Zebuloni, Dani ndi Nafitali.