Genesis 20:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tsopano Abulahamu anasamutsa msasa wake+ n’kupita kudziko la Negebu. Kenako anakakhala monga mlendo ku Gerari+ pakati pa Kadesi+ ndi Shura.+
20 Tsopano Abulahamu anasamutsa msasa wake+ n’kupita kudziko la Negebu. Kenako anakakhala monga mlendo ku Gerari+ pakati pa Kadesi+ ndi Shura.+