Salimo 33:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Hatchi siingabweretse chipulumutso,+Siingapulumutse munthu chifukwa cha kuchuluka kwa mphamvu zake.+ Miyambo 21:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Hatchi* anaikonzera tsiku la nkhondo,+ koma Yehova ndiye amapulumutsa.+
17 Hatchi siingabweretse chipulumutso,+Siingapulumutse munthu chifukwa cha kuchuluka kwa mphamvu zake.+