Yoswa 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Anatumizanso uthenga kwa mafumu amene anali m’dera lamapiri kumpoto, ndiponso m’chipululu kum’mwera kwa nyanja ya Kinereti,*+ mafumu a ku Sefela,+ ndiponso kwa mafumu okhala m’mapiri a Dori+ kumadzulo.
2 Anatumizanso uthenga kwa mafumu amene anali m’dera lamapiri kumpoto, ndiponso m’chipululu kum’mwera kwa nyanja ya Kinereti,*+ mafumu a ku Sefela,+ ndiponso kwa mafumu okhala m’mapiri a Dori+ kumadzulo.