Numeri 34:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Malirewo akatsike kuchokera ku Sefamu kulowera ku Ribila, kum’mawa kwa Aini. Akatsikebe mpaka akagunde malo otsetsereka a kum’mawa kwa nyanja ya Kinereti.*+
11 Malirewo akatsike kuchokera ku Sefamu kulowera ku Ribila, kum’mawa kwa Aini. Akatsikebe mpaka akagunde malo otsetsereka a kum’mawa kwa nyanja ya Kinereti.*+