1 Mafumu 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Choncho amisiri omanga a Solomo ndi amisiri omanga a Hiramu ndiponso Agebala+ anasema miyalayo, ndipo anapitiriza kudula mitengo ndi kusema miyala pokonzekera kumanga nyumbayo. Ezekieli 27:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Amuna achikulire a ku Gebala+ ndi anthu ake aluso anali mkati mwako monga anthu omata molumikizira matabwa ako.+ Zombo zonse zapanyanja ndi oziyendetsa anali mwa iwe kuti muchite malonda ndi kusinthana zinthu.
18 Choncho amisiri omanga a Solomo ndi amisiri omanga a Hiramu ndiponso Agebala+ anasema miyalayo, ndipo anapitiriza kudula mitengo ndi kusema miyala pokonzekera kumanga nyumbayo.
9 Amuna achikulire a ku Gebala+ ndi anthu ake aluso anali mkati mwako monga anthu omata molumikizira matabwa ako.+ Zombo zonse zapanyanja ndi oziyendetsa anali mwa iwe kuti muchite malonda ndi kusinthana zinthu.