Numeri 34:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Malirewo akatsike ndithu mpaka kumtsinje wa Yorodano, ndipo akathere ku Nyanja Yamchere.+ Limeneli ndilo dziko lanu+ ndi malire ake olizungulira.’”
12 Malirewo akatsike ndithu mpaka kumtsinje wa Yorodano, ndipo akathere ku Nyanja Yamchere.+ Limeneli ndilo dziko lanu+ ndi malire ake olizungulira.’”