Nehemiya 11:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ana ena a Yuda anali kukhala m’midzi ndi m’madera ozungulira midziyo.+ Ena anali kukhala ku Kiriyati-ariba+ ndi midzi yake yozungulira, ku Diboni* ndi midzi yake yozungulira, ku Yekabizeeli+ ndi midzi yake yozungulira,
25 Ana ena a Yuda anali kukhala m’midzi ndi m’madera ozungulira midziyo.+ Ena anali kukhala ku Kiriyati-ariba+ ndi midzi yake yozungulira, ku Diboni* ndi midzi yake yozungulira, ku Yekabizeeli+ ndi midzi yake yozungulira,