Genesis 23:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Sara anamwalirira ku Kiriyati-ariba,+ kapena kuti ku Heburoni,+ m’dziko la Kanani.+ Pamenepo Abulahamu analowa muhema kukamulira Sara. Yoswa 14:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Zimenezi zisanachitike, mzinda wa Heburoni unkatchedwa Kiriyati-ariba+ (Ariba+ anali munthu wamphamvu pakati pa Aanaki). Ndipo dziko lonse linakhala bata, lopanda nkhondo.+
2 Sara anamwalirira ku Kiriyati-ariba,+ kapena kuti ku Heburoni,+ m’dziko la Kanani.+ Pamenepo Abulahamu analowa muhema kukamulira Sara.
15 Zimenezi zisanachitike, mzinda wa Heburoni unkatchedwa Kiriyati-ariba+ (Ariba+ anali munthu wamphamvu pakati pa Aanaki). Ndipo dziko lonse linakhala bata, lopanda nkhondo.+