Genesis 38:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Patapita nthawi, mkazi wa Yuda, yemwe anali mwana wa Sua,+ anamwalira. Nthawi yolira maliro+ itatha Yuda anapita ku Timuna,+ kumene anyamata ake anali kumeta ubweya nkhosa zake. Anapita kumeneko limodzi ndi bwenzi lake Hira wachiadulamu+ uja.
12 Patapita nthawi, mkazi wa Yuda, yemwe anali mwana wa Sua,+ anamwalira. Nthawi yolira maliro+ itatha Yuda anapita ku Timuna,+ kumene anyamata ake anali kumeta ubweya nkhosa zake. Anapita kumeneko limodzi ndi bwenzi lake Hira wachiadulamu+ uja.