Yoswa 18:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Malirewo anapitirira kukafika ku Luzi,+ kutanthauza Beteli.+ Anakafika kum’mwera kwa malo otsetsereka otchedwa Luzi, n’kutsetserekera ku Ataroti-adara,+ n’kukadutsa paphiri la kum’mwera kwa Beti-horoni Wakumunsi.+ 1 Mbiri 7:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mwana wake wamkazi anali Seera, ndipo iye anamanga mzinda wa Beti-horoni,+ wakumunsi+ ndi wakumtunda.+ Anamanganso mzinda wa Uzeni-seera.
13 Malirewo anapitirira kukafika ku Luzi,+ kutanthauza Beteli.+ Anakafika kum’mwera kwa malo otsetsereka otchedwa Luzi, n’kutsetserekera ku Ataroti-adara,+ n’kukadutsa paphiri la kum’mwera kwa Beti-horoni Wakumunsi.+
24 Mwana wake wamkazi anali Seera, ndipo iye anamanga mzinda wa Beti-horoni,+ wakumunsi+ ndi wakumtunda.+ Anamanganso mzinda wa Uzeni-seera.