Yoswa 16:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Malire a kum’mawa a cholowa cha ana a Efuraimu potsata mabanja awo, anali Ataroti-adara+ mpaka kukafika ku Beti-horoni Wakumtunda,+ 2 Mbiri 8:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno anamanga mzinda wa Beti-horoni Wakumtunda+ ndi Beti-horoni Wakumunsi.+ Imeneyi inali mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri,+ zitseko ndi mipiringidzo.+
5 Malire a kum’mawa a cholowa cha ana a Efuraimu potsata mabanja awo, anali Ataroti-adara+ mpaka kukafika ku Beti-horoni Wakumtunda,+
5 Ndiyeno anamanga mzinda wa Beti-horoni Wakumtunda+ ndi Beti-horoni Wakumunsi.+ Imeneyi inali mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri,+ zitseko ndi mipiringidzo.+