Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 32:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ifeyo tinyamula zida zathu n’kufola mwa dongosolo lomenyera nkhondo+ ndipo titsogolera ana a Isiraeli kunkhondo mpaka tikawafikitse kumalo awo. Koma ana athu aang’ono tiwasiye m’mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri kuti tiwateteze kwa anthu a dziko lino.

  • Deuteronomo 28:52
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 52 Chotero adzakuzungulirani m’mizinda yanu yonse kufikira mipanda yanu yaitali ndi yolimba kwambiri imene muzidzaidalira itagwa m’dziko lanu lonse. Adzakuzungulirani ndithu m’mizinda yanu yonse m’dziko lanu limene Yehova Mulungu wanu wakupatsani.+

  • 2 Mafumu 10:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Inu muli ndi ana aamuna a mbuye wanu, magaleta ankhondo ndi mahatchi,+ ndiponso mzinda wokhala ndi mpanda wolimba kwambiri ndi zida zankhondo. Choncho mukangolandira kalatayi,

  • 2 Mbiri 12:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Sisakiyo analanda mizinda ya Yuda+ yomwe inali ndi mipanda yolimba kwambiri, ndipo pamapeto pake anafika ku Yerusalemu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena