Deuteronomo 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Chotero ndinakulamulani pa nthawi imeneyo kuti, ‘Yehova Mulungu wanu wakupatsani dzikoli kuti mulitenge kukhala lanu. Amuna nonse olimba mtima muwoloke, mukuyenda patsogolo pa abale anu, ana a Isiraeli, muli okonzeka ndi zida.+ Yoswa 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ana a Rubeni ndi ana a Gadi, ndi hafu ya fuko la Manase,+ anawoloka pamaso pa ana a Isiraeli atafola mwa dongosolo lomenyera nkhondo,+ monga mmene Mose anawauzira.+
18 “Chotero ndinakulamulani pa nthawi imeneyo kuti, ‘Yehova Mulungu wanu wakupatsani dzikoli kuti mulitenge kukhala lanu. Amuna nonse olimba mtima muwoloke, mukuyenda patsogolo pa abale anu, ana a Isiraeli, muli okonzeka ndi zida.+
12 Ana a Rubeni ndi ana a Gadi, ndi hafu ya fuko la Manase,+ anawoloka pamaso pa ana a Isiraeli atafola mwa dongosolo lomenyera nkhondo,+ monga mmene Mose anawauzira.+